Luso la Utumiki
bij 1 winkel
Verwant
Streepjescode: 9781643292304
Alle aanbiedingen
- bol.comLuso la UtumikiNaar de winkel€ 8,99Op voorraad
We verdienen mogelijk commissie als je via deze link koopt. Wat jij betaalt verandert niet.
Over dit product
Kukuza luso ndiko kukuza kuthekera. Baibulo limanena kuti kukonderedwa kumadza kwa anthu a luso. Ntchito ya utumiki imafuna kuthekera kwa kukulu. Bukhu latsopanoli, "Luso la Utumiki" ndi lofunika kwambiri kwa onse amene amakhumbira kuchita ntchito ya Mulungu. Limawonetseratu maganizo omwe ali olondola ndi oipa okhudzana ndi utumiki, chomwe ntchito ya utumiki chiri, chomwe mukuyenera kuchita ngati wogwira ntchito mu utumiki ndi momwe mungapangire ntchito za mtumiki. Mwadabwapo zokhuzana ndi momwe mungachitire ntchito ya utumiki? Bukhu lapaderali lolembedwa ndi Dag Heward-Mills likakulimbikitsani inu kuyenda moyenereza maitanidwe an a Mulungu ndi kukutsogozani inu mu kudzipereka nokha kwathunthu ku ntchito ya Mulungu.
Omschrijving aangeleverd door bol.com.