Aller au contenu
GiftCoves
Zomwe Zikutanthauza Kukhala M’busa

Zomwe Zikutanthauza Kukhala M’busa

7,49 €

dans 1 boutique

Code-barres: 9781643297385

Toutes les offres

Nous pouvons percevoir une commission si vous achetez via ce lien. Le prix que vous payez ne change pas.

À propos de ce produit

Chinthu chimodzi chokha chimadza kwa inu mukamva mawu akuti "M'busa" - nkhosa! Nkhosa ndi nyama zodalira zome zimafunikira abusa. M'busa ndi wotsogolera wosamalira komanso wachikondi kwa nkhosa. M'Baibulo, Mulungu amatitchula ife ngati gulu la nkhosa za Mulungu. Yesu adamuuza wophunzira Petro kuti adyetse nkhosa zake kuti atsimikizire za chikondi chake cha Mpulumutsi. Kukhala m'busa ndi ntchito yabwino kwambiri. Ndi chinthu chapamwamba kuitanidwa ndi Mulungu ndi kulembetsedwa mwa antchito Ake ndi kusamalira nkhosa. Mu bukhuli, Dag Heward-Mills akutiitanira ife, akutilimbikitsa ndi kutiwonetsa ife momwe tingatengerepo nawo mbali pa ntchito yayikulu yosamalira anthu a Mulungu. Musati muzisiyidwe kunja kwa ntchito yabwino iyi yokhala m'busa!

Description fournie par bol.com.

Se connecter

Indiquez votre adresse e-mail et nous vous enverrons un lien. Aucun mot de passe à retenir.

Continuer avec Google
ou